Umamva Bwanji-Maskal
DOLBY 杜比全景声 下载
臻品母带 下载
臻品全景声 下载
臻品音质
HIRES Hi-Res 下载
FLAC 无损flac 百度云网盘下载
APE 无损ape 格式下载
320MP3 极高mp3 歌曲下载
128MP3 标准mp3 百度网盘下载
192OGG 较高ogg 下载
192AAC 较高aac 下载
96AAC 标准aac 百度云下载
Loading...
TXT Umamva Bwanji-Maskal 文本歌词
ukakhala ndi ine baby
nthumazi imandigwira baby
nthawi zonse ukatalikira
ndimagwidwa ndi maganizo
ndimasowa chithandizo
ndidziwa bwanji za mtima mwako
poti udziwa wekha!
ukakhala ndi anzako
umawawuza chani za ine
umaganiza chani baby
ndiwuze ndidziwe
mu mtima mwako ndi ine
popeza unandidziwa
utapasidwanso mwayi osankha
ungasankhe ine!
ndiwuze ndidziwe eee
nkuthekatu zili bwino
unemkumati zili bwino
pali zambiri ndimafuna nditadziwa
umaganiza chani baby
ndiwuze ndi dziwe
Umamva Bwanji-Maskal 推荐歌曲
Umunthu专辑下载
(2013-12-05)